Salimo 33:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iye amakonda chilungamo ndi chiweruzo chosakondera.+Dziko lapansi ladzaza ndi kukoma mtima kosatha kwa Yehova.+ Salimo 67:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mitundu ya anthu isangalale ndi kufuula mokondwera,+Pakuti inu mudzaweruza anthu molungama.+Ndipo mudzatsogolera mitundu ya anthu padziko lapansi. [Seʹlah.] Danieli 4:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 “Tsopano ine Nebukadinezara ndikutamanda, kukweza ndi kulemekeza Mfumu yakumwamba,+ chifukwa ntchito zake zonse ndizo choonadi, njira zake ndi zolungama,+ ndiponso amatha kutsitsa anthu onyada.”+
5 Iye amakonda chilungamo ndi chiweruzo chosakondera.+Dziko lapansi ladzaza ndi kukoma mtima kosatha kwa Yehova.+
4 Mitundu ya anthu isangalale ndi kufuula mokondwera,+Pakuti inu mudzaweruza anthu molungama.+Ndipo mudzatsogolera mitundu ya anthu padziko lapansi. [Seʹlah.]
37 “Tsopano ine Nebukadinezara ndikutamanda, kukweza ndi kulemekeza Mfumu yakumwamba,+ chifukwa ntchito zake zonse ndizo choonadi, njira zake ndi zolungama,+ ndiponso amatha kutsitsa anthu onyada.”+