Yobu 37:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Wamphamvuyonse sitikumudziwa.+Iye ali ndi mphamvu zambiri,+Ndipo sadzanyoza+ chilungamo+ ndi kulungama kochuluka.+ Salimo 11:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pakuti Yehova ndi wolungama.+ Amakonda ntchito zolungama.+Anthu owongoka mtima ndi amene adzaona nkhope yake.+ Salimo 45:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Umakonda chilungamo+ ndipo umadana ndi zoipa.+N’chifukwa chake Mulungu, Mulungu wako,+ wakudzoza+ ndi mafuta achikondwerero chachikulu+ kuposa cha mafumu ena.+
23 Wamphamvuyonse sitikumudziwa.+Iye ali ndi mphamvu zambiri,+Ndipo sadzanyoza+ chilungamo+ ndi kulungama kochuluka.+
7 Pakuti Yehova ndi wolungama.+ Amakonda ntchito zolungama.+Anthu owongoka mtima ndi amene adzaona nkhope yake.+
7 Umakonda chilungamo+ ndipo umadana ndi zoipa.+N’chifukwa chake Mulungu, Mulungu wako,+ wakudzoza+ ndi mafuta achikondwerero chachikulu+ kuposa cha mafumu ena.+