Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mbiri 29:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Chotero, Solomo anayamba kukhala pampando wachifumu wa Yehova+ monga mfumu m’malo mwa Davide bambo wake, ndipo ankalamulira bwino.+ Aisiraeli onse anali kumumvera.

  • 2 Mbiri 13:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Kodi simukudziwa kuti Yehova Mulungu wa Isiraeli anapereka ufumu kwa Davide+ kuti azilamulira Isiraeli mpaka kalekale?+ Simukudziwa kodi kuti anaupereka kwa iye ndi ana ake+ pochita naye pangano losatha?*+

  • 2 Mbiri 13:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 “Tsopano anthu inu mukuganiza zolimbana ndi ufumu wa Yehova umene uli m’manja mwa ana a Davide,+ popeza ndinu khamu lalikulu+ ndipo muli ndi ana a ng’ombe agolide amene Yerobowamu anakupangirani kuti akhale milungu yanu.+

  • Mateyu 1:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Jese anabereka mfumu+ Davide.+

       Davide anabereka Solomo,+ yemwe mayi ake anali mkazi wa Uriya.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena