2 Samueli 7:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iye ndi amene adzamangira dzina langa nyumba,+ ndipo ndidzakhazikitsa mpando wake wachifumu mpaka kalekale.+ 1 Mbiri 17:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndidzamukhazikitsa iye kukhala woyang’anira nyumba yanga+ ndi ufumu wanga+ mpaka kalekale, ndipo mpando wake wachifumu+ sudzatha mpaka kalekale.”’”
13 Iye ndi amene adzamangira dzina langa nyumba,+ ndipo ndidzakhazikitsa mpando wake wachifumu mpaka kalekale.+
14 Ndidzamukhazikitsa iye kukhala woyang’anira nyumba yanga+ ndi ufumu wanga+ mpaka kalekale, ndipo mpando wake wachifumu+ sudzatha mpaka kalekale.”’”