1 Mafumu 1:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Monga momwe Yehova anakhalira ndi inu mbuyanga mfumu,+ akhalenso ndi Solomo+ ndipo achititse mpando wake wachifumu kukhala waukulu+ kuposa mpando wanu wachifumu, mbuyanga Mfumu Davide.” 1 Mbiri 28:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Akamatsatira malamulo anga+ ndi zigamulo zanga+ ndi mtima wonse ngati mmene akuchitira lero, ine ndidzakhazikitsa ufumu wake+ ndipo sudzagwedezeka mpaka kalekale.’ Salimo 89:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 ‘Ndidzakhazikitsa mbewu yako mpaka kalekale,+Ndipo ndidzalimbitsa mpando wako wachifumu+ ku mibadwomibadwo.’” [Seʹlah.] Salimo 89:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Mbewu yake idzakhala mpaka kalekale,+Ndipo mpando wake wachifumu udzakhala ngati dzuwa pamaso panga.+ Luka 1:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Iye adzalamulira monga mfumu panyumba ya Yakobo kwamuyaya, moti ufumu wake sudzatha konse.”+
37 Monga momwe Yehova anakhalira ndi inu mbuyanga mfumu,+ akhalenso ndi Solomo+ ndipo achititse mpando wake wachifumu kukhala waukulu+ kuposa mpando wanu wachifumu, mbuyanga Mfumu Davide.”
7 Akamatsatira malamulo anga+ ndi zigamulo zanga+ ndi mtima wonse ngati mmene akuchitira lero, ine ndidzakhazikitsa ufumu wake+ ndipo sudzagwedezeka mpaka kalekale.’
4 ‘Ndidzakhazikitsa mbewu yako mpaka kalekale,+Ndipo ndidzalimbitsa mpando wako wachifumu+ ku mibadwomibadwo.’” [Seʹlah.]
36 Mbewu yake idzakhala mpaka kalekale,+Ndipo mpando wake wachifumu udzakhala ngati dzuwa pamaso panga.+