2 Samueli 7:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Masiku ako akadzakwana,+ ndipo ukadzagona pamodzi ndi makolo ako,+ pamenepo ndidzautsa mbewu yako yobwera pambuyo pako, imene idzatuluka m’chiuno mwako. Ndipo ndidzakhazikitsadi ufumu wake.+ 1 Mbiri 17:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “‘“Masiku ako akadzakwana kuti ukakhale pamodzi ndi makolo ako,+ pamenepo ndithu ndidzautsa mbewu yako yobwera pambuyo pako,+ imene idzakhala mmodzi wa ana ako, ndipo ndidzakhazikitsadi ufumu wake.+ Chivumbulutso 22:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “‘Ine Yesu, ndinatumiza mngelo wanga kudzachitira umboni zinthu izi kwa inu, kuti zithandize mipingo. Ine ndine muzu+ ndi mbadwa+ ya Davide. Ndinenso nthanda yonyezimira.’”+
12 Masiku ako akadzakwana,+ ndipo ukadzagona pamodzi ndi makolo ako,+ pamenepo ndidzautsa mbewu yako yobwera pambuyo pako, imene idzatuluka m’chiuno mwako. Ndipo ndidzakhazikitsadi ufumu wake.+
11 “‘“Masiku ako akadzakwana kuti ukakhale pamodzi ndi makolo ako,+ pamenepo ndithu ndidzautsa mbewu yako yobwera pambuyo pako,+ imene idzakhala mmodzi wa ana ako, ndipo ndidzakhazikitsadi ufumu wake.+
16 “‘Ine Yesu, ndinatumiza mngelo wanga kudzachitira umboni zinthu izi kwa inu, kuti zithandize mipingo. Ine ndine muzu+ ndi mbadwa+ ya Davide. Ndinenso nthanda yonyezimira.’”+