Deuteronomo 31:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Tsopano Yehova anauza Mose kuti: “Iweyo ugona pamodzi ndi makolo ako,+ ndipo anthu awa adzaimirira+ ndi kuchita chiwerewere pakati pawo ndi milungu yachilendo ya m’dziko limene akupita.+ Iwo adzandisiya+ ndi kuphwanya pangano limene ndinapangana nawo.+ 1 Mafumu 1:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Zomwe zidzachitike n’zoti, inuyo mbuyanga mfumu mukadzangogona m’manda limodzi ndi makolo anu,+ ineyo ndi mwana wanga Solomo tidzaoneka ngati olakwa.” Machitidwe 13:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Koma Davide+ anakwaniritsa chifuniro cha Mulungu mu nthawi ya m’badwo wake, ndipo anagona mu imfa ndi kuikidwa m’manda pamodzi ndi makolo ake, moti thupi lake linavunda.+
16 Tsopano Yehova anauza Mose kuti: “Iweyo ugona pamodzi ndi makolo ako,+ ndipo anthu awa adzaimirira+ ndi kuchita chiwerewere pakati pawo ndi milungu yachilendo ya m’dziko limene akupita.+ Iwo adzandisiya+ ndi kuphwanya pangano limene ndinapangana nawo.+
21 Zomwe zidzachitike n’zoti, inuyo mbuyanga mfumu mukadzangogona m’manda limodzi ndi makolo anu,+ ineyo ndi mwana wanga Solomo tidzaoneka ngati olakwa.”
36 Koma Davide+ anakwaniritsa chifuniro cha Mulungu mu nthawi ya m’badwo wake, ndipo anagona mu imfa ndi kuikidwa m’manda pamodzi ndi makolo ake, moti thupi lake linavunda.+