Genesis 15:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kunena za iweyo, udzatsikira kwa makolo ako mu mtendere. Udzaikidwa m’manda uli wokalamba, utakhala ndi moyo wabwino ndi wautali.+ 1 Mafumu 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kenako Davide anagona limodzi ndi makolo ake,+ ndipo anaikidwa m’manda mu Mzinda wa Davide.+
15 Kunena za iweyo, udzatsikira kwa makolo ako mu mtendere. Udzaikidwa m’manda uli wokalamba, utakhala ndi moyo wabwino ndi wautali.+