Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 5:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ngakhale zinali choncho, Davide analanda Ziyoni, malo okhala mumpanda wolimba kwambiri,+ umene ndi Mzinda wa Davide.+

  • 1 Mafumu 3:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Kenako Solomo anachita mgwirizano wa ukwati+ ndi Farao mfumu ya Iguputo. Anatenga mwana wamkazi wa Faraoyo+ n’kubwera naye ku Mzinda wa Davide,+ kuti azikhala kaye kumeneko mpaka iye atamaliza kumanga nyumba yake,+ nyumba ya Yehova,+ ndi mpanda wozungulira Yerusalemu yense.+

  • 1 Mafumu 11:43
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 43 Kenako Solomo anagona pamodzi ndi makolo ake,+ ndipo anaikidwa m’manda mu Mzinda wa Davide+ bambo ake. Kenako mwana wake Rehobowamu,+ anayamba kulamulira m’malo mwake.

  • 1 Mbiri 11:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ndiyeno Davide anayamba kukhala m’malo ovuta kufikako.+ N’chifukwa chake mzindawo anautcha kuti Mzinda wa Davide.+

  • Machitidwe 2:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 “Amuna inu, abale anga, ndilankhula ndithu mwaufulu za kholo lathu Davide. Iye anamwalira+ ndi kuikidwa m’manda, ndipo manda ake tili nawo mpaka lero.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena