2 Samueli 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ngakhale zinali choncho, Davide analanda Ziyoni, malo okhala mumpanda wolimba kwambiri,+ umene ndi Mzinda wa Davide.+ 1 Mbiri 11:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno Davide anayamba kukhala m’malo ovuta kufikako.+ N’chifukwa chake mzindawo anautcha kuti Mzinda wa Davide.+
7 Ngakhale zinali choncho, Davide analanda Ziyoni, malo okhala mumpanda wolimba kwambiri,+ umene ndi Mzinda wa Davide.+
7 Ndiyeno Davide anayamba kukhala m’malo ovuta kufikako.+ N’chifukwa chake mzindawo anautcha kuti Mzinda wa Davide.+