-
2 Samueli 12:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Tsopano sonkhanitsani anthu otsalawo kuti muuthire nkhondo mzindawu ndi kuulanda, kuti ndisaulande ndine, kuopera kuti lingatchuke ndi dzina langa.”
-