28 Pamapeto pake, iye anamwalira ali wokalamba, atakhala ndi moyo wabwino ndi wautali,+ wokhutira ndi masiku, chuma+ ndi ulemerero.+ Kenako Solomo mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.+
36 Koma Davide+ anakwaniritsa chifuniro cha Mulungu mu nthawi ya m’badwo wake, ndipo anagona mu imfa ndi kuikidwa m’manda pamodzi ndi makolo ake, moti thupi lake linavunda.+