1 Mafumu 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Davide atatsala pang’ono kumwalira,+ anaitana mwana wake Solomo n’kumulamula kuti: 1 Mafumu 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kenako Davide anagona limodzi ndi makolo ake,+ ndipo anaikidwa m’manda mu Mzinda wa Davide.+ 1 Mafumu 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Solomo anakhala pampando wachifumu wa Davide bambo ake,+ ndipo m’kupita kwa nthawi, ufumu wake unakhazikika.+
12 Solomo anakhala pampando wachifumu wa Davide bambo ake,+ ndipo m’kupita kwa nthawi, ufumu wake unakhazikika.+