1 Mafumu 1:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Komanso, Solomo wakhala pampando wachifumu.+ 1 Mbiri 29:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Chotero, Solomo anayamba kukhala pampando wachifumu wa Yehova+ monga mfumu m’malo mwa Davide bambo wake, ndipo ankalamulira bwino.+ Aisiraeli onse anali kumumvera. 2 Mbiri 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Solomo mwana wa Davide anapitiriza kukhala wamphamvu mu ufumu wake.+ Yehova Mulungu wake anali naye,+ ndipo anapitiriza kumukulitsa kuposa wina aliyense.+ Salimo 132:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ana ako akadzasunga pangano langa+Ndi zikumbutso zanga zimene ndidzawapatsa,+Ngakhalenso ana awo+Adzakhala pampando wako wachifumu kwamuyaya.”+
23 Chotero, Solomo anayamba kukhala pampando wachifumu wa Yehova+ monga mfumu m’malo mwa Davide bambo wake, ndipo ankalamulira bwino.+ Aisiraeli onse anali kumumvera.
1 Solomo mwana wa Davide anapitiriza kukhala wamphamvu mu ufumu wake.+ Yehova Mulungu wake anali naye,+ ndipo anapitiriza kumukulitsa kuposa wina aliyense.+
12 Ana ako akadzasunga pangano langa+Ndi zikumbutso zanga zimene ndidzawapatsa,+Ngakhalenso ana awo+Adzakhala pampando wako wachifumu kwamuyaya.”+