Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 3:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ndikupatsanso zomwe sunapemphe,+ chuma+ ndi ulemerero, moti sikudzakhalanso mfumu ngati iwe masiku ako onse.+

  • 1 Mbiri 29:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Yehova anapitiriza kukweza Solomo+ pamaso pa Aisiraeli onse, ndi kum’patsa ulemu waukulu wachifumu kuposa mfumu ina iliyonse imene inalamulira Isiraeli iye asanakhale mfumu.+

  • Mlaliki 2:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ndinali ndi zinthu zambiri kuposa aliyense amene anakhalapo mu Yerusalemu ine ndisanakhalepo.+ Komanso ndinali kuchitabe zinthu mwanzeru.+

  • Mateyu 6:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Komatu ndikukuuzani kuti ngakhale Solomo+ mu ulemerero wake wonse sanavalepo zokongola ngati lililonse la maluwa amenewa.

  • Mateyu 12:42
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 42 Mfumukazi ya kum’mwera+ adzaiukitsa kwa akufa limodzi ndi m’badwo uwu ndipo idzautsutsa, chifukwa mfumukazi imeneyi inabwera kuchokera kumalekezero a dziko lapansi kudzamva nzeru za Solomo. Koma tsopano wina woposa Solomo ali pano.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena