1 Mafumu 4:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Solomo anakhala wolamulira wa maufumu onse kuyambira ku Mtsinje*+ mpaka kudziko la Afilisiti, n’kukafika kumalire ndi Iguputo. Maufumu amenewa anali kubweretsa mphatso kwa Solomo ndi kum’tumikira masiku onse a moyo wake.+ Miyambo 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Masiku ochuluka ali m’dzanja lake lamanja.+ M’dzanja lake lamanzere muli chuma ndi ulemerero.+ Mlaliki 7:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Munthu wanzeru akalandira cholowa zimakhala bwino, ndipo nzeru zimapindulitsa anthu amene ali padziko lapansi.+
21 Solomo anakhala wolamulira wa maufumu onse kuyambira ku Mtsinje*+ mpaka kudziko la Afilisiti, n’kukafika kumalire ndi Iguputo. Maufumu amenewa anali kubweretsa mphatso kwa Solomo ndi kum’tumikira masiku onse a moyo wake.+
11 Munthu wanzeru akalandira cholowa zimakhala bwino, ndipo nzeru zimapindulitsa anthu amene ali padziko lapansi.+