1 Mafumu 10:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Chotero Mfumu Solomo inali yolemera kwambiri+ ndiponso yanzeru+ kwambiri kuposa mafumu ena onse a padziko lapansi. 2 Mbiri 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 upatsidwa nzeru ndi luntha lodziwa zinthu.+ Ndikupatsanso katundu, chuma, ndi ulemu zochuluka kwambiri kuposa zimene anali nazo mafumu amene anakhalako iwe usanakhale,+ ndiponso zoposa zimene aliyense wobwera pambuyo pako adzakhale nazo.”+
23 Chotero Mfumu Solomo inali yolemera kwambiri+ ndiponso yanzeru+ kwambiri kuposa mafumu ena onse a padziko lapansi.
12 upatsidwa nzeru ndi luntha lodziwa zinthu.+ Ndikupatsanso katundu, chuma, ndi ulemu zochuluka kwambiri kuposa zimene anali nazo mafumu amene anakhalako iwe usanakhale,+ ndiponso zoposa zimene aliyense wobwera pambuyo pako adzakhale nazo.”+