1 Mafumu 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 taona, ndichita mogwirizanadi ndi mawu ako.+ Ndithu ndikupatsa mtima wanzeru ndi womvetsa zinthu+ moti ndi kale lonse sipanakhalepo munthu ngati iwe, ndipo pambuyo pako sipadzakhalanso wina ngati iwe.+ Salimo 34:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mikango yamphamvu ingakhale ndi chakudya chochepa ndipo ingamve njala.+Koma ofunafuna Yehova sadzasowa chilichonse chabwino.+ Aefeso 3:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tsopano kwa iye amene angathe kuchita zazikulu kwambiri kuposa zonse zimene timapempha kapena kuganiza,+ malinga ndi mphamvu yake imene ikugwira ntchito+ mwa ife, 1 Yohane 5:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Komanso, popeza timadziwa kuti amatimvera tikapempha chilichonse,+ timakhala ndi chikhulupiriro kuti tilandira zinthu zimene tamupemphazo.+
12 taona, ndichita mogwirizanadi ndi mawu ako.+ Ndithu ndikupatsa mtima wanzeru ndi womvetsa zinthu+ moti ndi kale lonse sipanakhalepo munthu ngati iwe, ndipo pambuyo pako sipadzakhalanso wina ngati iwe.+
10 Mikango yamphamvu ingakhale ndi chakudya chochepa ndipo ingamve njala.+Koma ofunafuna Yehova sadzasowa chilichonse chabwino.+
20 Tsopano kwa iye amene angathe kuchita zazikulu kwambiri kuposa zonse zimene timapempha kapena kuganiza,+ malinga ndi mphamvu yake imene ikugwira ntchito+ mwa ife,
15 Komanso, popeza timadziwa kuti amatimvera tikapempha chilichonse,+ timakhala ndi chikhulupiriro kuti tilandira zinthu zimene tamupemphazo.+