Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 4:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Mulungu anapitiriza kupatsa Solomo nzeru zopanda malire ndi luso lomvetsa zinthu losaneneka.+ Anam’patsanso mtima wozindikira zinthu mwakuya.+

  • 1 Mafumu 5:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ndiyeno Yehova anapatsa Solomo nzeru monga mmene anam’lonjezera.+ Pakati pa Hiramu ndi Solomo panali mtendere, ndipo awiriwa anachita pangano.

  • 2 Mbiri 1:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Pamenepo Mulungu anauza Solomo kuti: “Chifukwa chakuti zimenezi ndi zimene zili mumtima mwako+ ndipo sunapemphe katundu, chuma ndi ulemu kapenanso moyo wa anthu amene amadana nawe, sunapemphenso kuti ukhale ndi moyo masiku ambiri,+ koma wapempha kuti ukhale ndi nzeru ndi luntha lodziwa zinthu kuti uweruze anthu anga amene ndakupatsa kuti ukhale mfumu yawo,+

  • Miyambo 3:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Wodala ndi munthu amene wapeza nzeru,+ ndiponso munthu amene wapeza kuzindikira,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena