Genesis 41:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Yosefe anapitiriza kusunga tirigu, mpaka anachuluka kwambiri+ ngati mchenga wa kunyanja. Tiriguyo anachuluka kwadzaoneni, moti sanathenso kumamuyeza chifukwa cha kuchuluka kwake.+ Salimo 119:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ndidzamvera malamulo anu,+Chifukwa mwandichititsa kuwamvetsa bwino.+
49 Yosefe anapitiriza kusunga tirigu, mpaka anachuluka kwambiri+ ngati mchenga wa kunyanja. Tiriguyo anachuluka kwadzaoneni, moti sanathenso kumamuyeza chifukwa cha kuchuluka kwake.+