Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 10:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Mudzamva kuchonderera kwa anthu ofatsa,+ inu Yehova.

      Mudzakonzekeretsa mitima yawo.+

      Mudzatchera khutu lanu,+

  • Mlaliki 1:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Ineyo ndinanena mumtima mwanga+ kuti: “Ine ndili ndi nzeru zambiri kuposa aliyense amene anakhalapo mu Yerusalemu ine ndisanakhalepo.+ Komanso mtima wanga wapeza nzeru zambiri ndiponso wadziwa zinthu zambiri.”+

  • Yesaya 65:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Iwo asanandiitane, ine ndidzayankha.+ Asanamalize kulankhula, ine ndidzamva.+

  • 1 Yohane 5:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ifetu timamudalira+ kuti chilichonse chimene tingamupemphe mogwirizana ndi chifuniro chake, amatimvera.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena