1 Samueli 8:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Samueli anamvera mawu onse amene anthuwo ananena, kenako anafotokozera Yehova mawuwo.+ Salimo 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yehova adzamva ndithu pempho langa loti andikomere mtima.+Yehova adzalandira pemphero langa.+ Salimo 9:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pakuti waumphawi sadzaiwalidwa nthawi zonse,+Ndiponso chiyembekezo cha ofatsa sichidzatha konse.+ Salimo 102:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Iye adzamvetsera pemphero la anthu amene alandidwa chilichonse,+Ndipo sadzapeputsa pemphero lawo.+ Miyambo 15:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Nsembe ya anthu oipa imam’nyansa Yehova,+ koma pemphero la anthu owongoka mtima limam’sangalatsa.+ 1 Petulo 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pakuti maso+ a Yehova* ali pa olungama, ndipo makutu ake amamva pembedzero lawo,+ koma nkhope ya Yehova imakwiyira anthu ochita zoipa.”+ 1 Yohane 3:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 ndipo chilichonse chimene tingapemphe, iye adzatipatsa,+ chifukwa tikusunga malamulo ake ndi kuchita zinthu zomukondweretsa.+
17 Iye adzamvetsera pemphero la anthu amene alandidwa chilichonse,+Ndipo sadzapeputsa pemphero lawo.+
12 Pakuti maso+ a Yehova* ali pa olungama, ndipo makutu ake amamva pembedzero lawo,+ koma nkhope ya Yehova imakwiyira anthu ochita zoipa.”+
22 ndipo chilichonse chimene tingapemphe, iye adzatipatsa,+ chifukwa tikusunga malamulo ake ndi kuchita zinthu zomukondweretsa.+