Salimo 31:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma ine nditapanikizika ndinati:+“Ndidzafafanizidwa kuchoka pamaso panu.”+Ndithudi mwamva kuchonderera kwanga pamene ndinali kufuulira kwa inu kupempha thandizo.+ Salimo 40:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Ndinayembekezera Yehova ndi mtima wonse,+Choncho iye anatchera khutu kwa ine ndipo anamva kufuula kwanga kopempha thandizo.+ Yona 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 kuti:“Pamene ndinali m’masautso ndinaitana Yehova,+ ndipo anandiyankha.+Ndinafuula kupempha thandizo ndili m’Manda* akuya.+Ndipo inu munamva mawu anga.+
22 Koma ine nditapanikizika ndinati:+“Ndidzafafanizidwa kuchoka pamaso panu.”+Ndithudi mwamva kuchonderera kwanga pamene ndinali kufuulira kwa inu kupempha thandizo.+
40 Ndinayembekezera Yehova ndi mtima wonse,+Choncho iye anatchera khutu kwa ine ndipo anamva kufuula kwanga kopempha thandizo.+
2 kuti:“Pamene ndinali m’masautso ndinaitana Yehova,+ ndipo anandiyankha.+Ndinafuula kupempha thandizo ndili m’Manda* akuya.+Ndipo inu munamva mawu anga.+