Salimo 88:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mafunde a mkwiyo wanu woyaka moto andimiza.+Zinthu zochititsa mantha zochokera kwa inu zandisowetsa chonena.+ Maliro 3:54 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 54 Madzi asefukira ndi kumiza mutu wanga,+ moti ndanena kuti: “Ndifa basi!”+ Yona 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndipo ine ndinati, ‘Mwandipitikitsa pamaso panu!+Kodi kachisi wanu woyera ndidzamuonanso?’+
16 Mafunde a mkwiyo wanu woyaka moto andimiza.+Zinthu zochititsa mantha zochokera kwa inu zandisowetsa chonena.+