Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 8:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 ndiyeno anthuwo akapereka pemphero lililonse,+ pempho lililonse lopempha chifundo+ limene munthu aliyense kapena anthu anu onse Aisiraeli angapemphe,+ chifukwa aliyense wa iwo akudziwa ululu wa mumtima mwake,+ ndipo iwo akatambasula manja awo kuwalozetsa kunyumba ino,+

  • 2 Mbiri 6:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 n’kubwerera kwa inu ndi mtima wawo wonse+ ndi moyo wawo wonse, m’dziko limene akukhalamo monga anthu ogwidwa,+ m’dziko la adani awo amene anawagwira ndiponso akapemphera kwa inu atayang’ana kudziko lawo limene munapatsa makolo awo, kumzinda umene mwasankha+ ndiponso kunyumba ya dzina lanu imene ndamangayi,+

  • Salimo 5:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Koma ine ndidzalowa m’nyumba yanu+

      Chifukwa cha kuchuluka kwa kukoma mtima kwanu kosatha.+

      Ndidzawerama nditayang’ana kumene kuli kachisi wanu wopatulika chifukwa chokuopani.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena