Salimo 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti simudzasiya moyo wanga m’Manda.+Simudzalola kuti wokhulupirika wanu aone dzenje.+ Mateyu 12:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Pakuti monga momwe Yona+ anakhalira m’mimba mwa chinsomba chachikulu masiku atatu, usana ndi usiku, chimodzimodzinso Mwana wa munthu+ adzakhala mumtima wa dziko lapansi+ masiku atatu, usana ndi usiku.+ Machitidwe 2:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 chifukwa simudzasiya moyo wanga m’Manda,* ndipo simudzalola kuti thupi la wokhulupirika wanu livunde.+
40 Pakuti monga momwe Yona+ anakhalira m’mimba mwa chinsomba chachikulu masiku atatu, usana ndi usiku, chimodzimodzinso Mwana wa munthu+ adzakhala mumtima wa dziko lapansi+ masiku atatu, usana ndi usiku.+
27 chifukwa simudzasiya moyo wanga m’Manda,* ndipo simudzalola kuti thupi la wokhulupirika wanu livunde.+