Yona 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Tsopano Yehova anatumiza chinsomba chachikulu kuti chikameze Yona,+ moti Yona anakhala m’mimba mwa nsomba masiku atatu, usana ndi usiku.+
17 Tsopano Yehova anatumiza chinsomba chachikulu kuti chikameze Yona,+ moti Yona anakhala m’mimba mwa nsomba masiku atatu, usana ndi usiku.+