Mateyu 12:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Pakuti monga momwe Yona+ anakhalira m’mimba mwa chinsomba chachikulu masiku atatu, usana ndi usiku, chimodzimodzinso Mwana wa munthu+ adzakhala mumtima wa dziko lapansi+ masiku atatu, usana ndi usiku.+ Mateyu 16:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 M’badwo woipa ndi wachigololo ukufunitsitsabe chizindikiro, koma sudzapatsidwa chizindikiro chilichonse+ kupatulapo chizindikiro cha Yona chokha.”+ Atanena izi, anachoka n’kuwasiya.+ Luka 11:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Monga momwe Yona+ anakhalira chizindikiro kwa anthu a ku Nineve, Mwana wa munthu adzakhalanso chizindikiro ku m’badwo uwu.
40 Pakuti monga momwe Yona+ anakhalira m’mimba mwa chinsomba chachikulu masiku atatu, usana ndi usiku, chimodzimodzinso Mwana wa munthu+ adzakhala mumtima wa dziko lapansi+ masiku atatu, usana ndi usiku.+
4 M’badwo woipa ndi wachigololo ukufunitsitsabe chizindikiro, koma sudzapatsidwa chizindikiro chilichonse+ kupatulapo chizindikiro cha Yona chokha.”+ Atanena izi, anachoka n’kuwasiya.+
30 Monga momwe Yona+ anakhalira chizindikiro kwa anthu a ku Nineve, Mwana wa munthu adzakhalanso chizindikiro ku m’badwo uwu.