Mateyu 12:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Poyankha iye anawauza kuti: “M’badwo woipa ndi wachigololo+ ukufunitsitsabe chizindikiro. Sudzapatsidwa chizindikiro chilichonse koma chizindikiro cha mneneri Yona chokha.+ Luka 11:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Pamene anthu osonkhana pamodzi anali kuchulukirachulukira, iye anayamba kunena kuti: “M’badwo uwu ndi m’badwo woipa, ukufuna chizindikiro.+ Koma sudzapatsidwa chizindikiro chilichonse kupatulapo chizindikiro cha Yona chokha.+
39 Poyankha iye anawauza kuti: “M’badwo woipa ndi wachigololo+ ukufunitsitsabe chizindikiro. Sudzapatsidwa chizindikiro chilichonse koma chizindikiro cha mneneri Yona chokha.+
29 Pamene anthu osonkhana pamodzi anali kuchulukirachulukira, iye anayamba kunena kuti: “M’badwo uwu ndi m’badwo woipa, ukufuna chizindikiro.+ Koma sudzapatsidwa chizindikiro chilichonse kupatulapo chizindikiro cha Yona chokha.+