Mateyu 16:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 M’badwo woipa ndi wachigololo ukufunitsitsabe chizindikiro, koma sudzapatsidwa chizindikiro chilichonse+ kupatulapo chizindikiro cha Yona chokha.”+ Atanena izi, anachoka n’kuwasiya.+
4 M’badwo woipa ndi wachigololo ukufunitsitsabe chizindikiro, koma sudzapatsidwa chizindikiro chilichonse+ kupatulapo chizindikiro cha Yona chokha.”+ Atanena izi, anachoka n’kuwasiya.+