Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 49:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Koma Mulungu adzawombola moyo wanga ku Manda,+

      Pakuti adzandilandira. [Seʹlah.]

  • Miyambo 15:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Manda ndiponso malo a chiwonongeko+ zili pamaso pa Yehova.+ Ndiye kuli bwanji mitima ya ana a anthu?+

  • Machitidwe 2:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Choncho pokhala mneneri, iye anaoneratu zapatsogolo ndi kuneneratu za kuuka kwa Khristu. Ananeneratu kuti iye sanasiyidwe m’Manda, komanso kuti thupi lake silinavunde.+

  • Machitidwe 3:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Chotero munapha Mtumiki Wamkulu wa moyo,+ koma Mulungu anamuukitsa kwa akufa, ndipo ife ndife mboni za choonadi chimenechi.+

  • Chivumbulutso 1:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 ndiponso wamoyo.+ Ndinali wakufa,+ koma taona, ndili ndi moyo kwamuyaya,+ ndipo ndili ndi makiyi a imfa+ ndi a Manda.*+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena