Salimo 88:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kodi adzalengeza za kukoma mtima kwanu kosatha m’manda?Kodi adzalengeza za kukhulupirika kwanu m’malo a chiwonongeko?+ Miyambo 27:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Manda ndiponso malo a chiwonongeko+ sakhuta.+ Nawonso maso a munthu sakhuta.+
11 Kodi adzalengeza za kukoma mtima kwanu kosatha m’manda?Kodi adzalengeza za kukhulupirika kwanu m’malo a chiwonongeko?+