Miyambo 27:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Manda ndiponso malo achiwonongeko* sakhuta,+Nawonso maso a munthu sakhuta. Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 27:20 Galamukani!,4/8/1999, tsa. 20