Machitidwe 5:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ameneyo Mulungu anamukweza kudzanja lake lamanja+ monga Mtumiki Wamkulu+ ndi Mpulumutsi.+ Anachita zimenezi kuti Aisiraeli alape+ ndi kuti machimo awo akhululukidwe.+ Aheberi 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Zinthu zonse zilipo kuti zipereke ulemerero kwa Mulungu ndipo zinakhalapo kudzera mwa iye.+ Choncho pamene akuika ana ambiri pa ulemerero,+ n’koyenera kuti achititse Mtumiki Wamkulu+ wa chipulumutso chawo kukhala wangwiro kudzera m’masautso.+
31 Ameneyo Mulungu anamukweza kudzanja lake lamanja+ monga Mtumiki Wamkulu+ ndi Mpulumutsi.+ Anachita zimenezi kuti Aisiraeli alape+ ndi kuti machimo awo akhululukidwe.+
10 Zinthu zonse zilipo kuti zipereke ulemerero kwa Mulungu ndipo zinakhalapo kudzera mwa iye.+ Choncho pamene akuika ana ambiri pa ulemerero,+ n’koyenera kuti achititse Mtumiki Wamkulu+ wa chipulumutso chawo kukhala wangwiro kudzera m’masautso.+