Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 6:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 inuyo mumve muli kumwamba, malo anu okhala okhazikika,+ ndipo mukhululuke+ ndi kuchitapo kanthu. Mupatse aliyense malinga ndi njira zake zonse,+ popeza mukudziwa mtima wake+ (popeza inu nokha ndiye mumadziwa bwino mtima wa ana a anthu).+

  • Salimo 7:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Chonde, thetsani kuipa kwa anthu oipa,+

      Ndipo khazikitsani wolungama.+

      Mulungu pokhala wolungama+ akuyesa mtima+ ndi impso.+

  • Salimo 44:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Kodi Mulungu sakanafufuza zimenezi?+

      Pakuti iye amadziwa zinsinsi za mumtima.+

  • Yeremiya 17:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ine Yehova ndimafufuza mtima+ ndi kusanthula impso.+ Munthu aliyense ndimamuchitira zinthu monga mwa zochita zake,+ mogwirizana ndi zipatso za ntchito zake.+

  • Machitidwe 1:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Ndipo anapemphera kuti: “Ambuye wathu Yehova, inu amene mumadziwa mitima ya anthu onse,+ tisonyezeni amene inu mwamusankha mwa amuna awiriwa,

  • Aheberi 4:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Palibe cholengedwa chimene Mulungu sangathe kuchiona.+ Chifukwa kwa iye zinthu zonse zili poonekera ndipo amatha kuziona bwinobwino. Ndipotu ife tikuyenera kudzayankha pa zochita zathu kwa Mulungu amene amaona zonseyo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena