Yeremiya 17:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ine Yehova ndimafufuza mtima,+Ndimafufuza maganizo a mkati mwa mtima wa munthu,*Kuti munthu aliyense ndimuchitire zinthu mogwirizana ndi zochita zake,Komanso mogwirizana ndi zipatso za ntchito zake.+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:10 Nsanja ya Olonda,3/15/2013, tsa. 9
10 Ine Yehova ndimafufuza mtima,+Ndimafufuza maganizo a mkati mwa mtima wa munthu,*Kuti munthu aliyense ndimuchitire zinthu mogwirizana ndi zochita zake,Komanso mogwirizana ndi zipatso za ntchito zake.+