Yobu 34:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti iye amapereka mphoto kwa munthu wochokera kufumbi malinga ndi zochita zake,+Ndipo amam’bweretsera zinthu zogwirizana ndi njira yake. Salimo 18:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Yehova amandipatsa mphoto mogwirizana ndi chilungamo changa.+Amandibwezera mogwirizana ndi kuyera kwa manja anga.+ Chivumbulutso 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ana ake ndidzawapha ndi mliri wakupha, moti mipingo yonse idzadziwa kuti ineyo ndiye amene ndimafufuza impso ndi mitima, ndipo ndidzabwezera mmodzi ndi mmodzi wa inu malinga ndi ntchito zake.+
11 Pakuti iye amapereka mphoto kwa munthu wochokera kufumbi malinga ndi zochita zake,+Ndipo amam’bweretsera zinthu zogwirizana ndi njira yake.
20 Yehova amandipatsa mphoto mogwirizana ndi chilungamo changa.+Amandibwezera mogwirizana ndi kuyera kwa manja anga.+
23 Ana ake ndidzawapha ndi mliri wakupha, moti mipingo yonse idzadziwa kuti ineyo ndiye amene ndimafufuza impso ndi mitima, ndipo ndidzabwezera mmodzi ndi mmodzi wa inu malinga ndi ntchito zake.+