Mateyu 16:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pakuti Mwana wa munthu adzabwera ndithu mu ulemerero wa Atate wake limodzi ndi angelo ake. Pa nthawi imeneyo adzapatsa aliyense mphoto malinga ndi makhalidwe ake.+ Chivumbulutso 22:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “‘Taonani! Ndikubwera mofulumira,+ ndipo mphoto+ ndili nayo, yoti ndipereke kwa aliyense malinga ndi ntchito yake.+
27 Pakuti Mwana wa munthu adzabwera ndithu mu ulemerero wa Atate wake limodzi ndi angelo ake. Pa nthawi imeneyo adzapatsa aliyense mphoto malinga ndi makhalidwe ake.+
12 “‘Taonani! Ndikubwera mofulumira,+ ndipo mphoto+ ndili nayo, yoti ndipereke kwa aliyense malinga ndi ntchito yake.+