Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 31:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ndiye ndingatani Mulungu akaimirira,

      Ndipo akandifunsa ndingamuyankhe chiyani?+

  • Machitidwe 17:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Chifukwa wakhazikitsa tsiku limene akufuna kudzaweruza+ m’chilungamo dziko lapansi kumene kuli anthu, kudzera mwa munthu amene iye wamuika. Ndipo wapereka chitsimikizo kwa anthu onse mwa kumuukitsa+ kwa akufa.”

  • Aroma 2:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Zimenezi zidzaonekera pa tsiku limene Mulungu, kudzera mwa Khristu Yesu, adzaweruze+ zinthu zobisika+ za anthu,+ mogwirizana ndi uthenga wabwino umene ndikulengeza.+

  • Aroma 14:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Chotero aliyense wa ife adzayankha yekha kwa Mulungu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena