Aroma 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Zimenezi zidzaonekera pa tsiku limene Mulungu, kudzera mwa Khristu Yesu, adzaweruze zinthu zachinsinsi zimene anthu amachita komanso kuganiza.+ Ndipo adzaweruza mogwirizana ndi uthenga wabwino umene ndikulalikira.
16 Zimenezi zidzaonekera pa tsiku limene Mulungu, kudzera mwa Khristu Yesu, adzaweruze zinthu zachinsinsi zimene anthu amachita komanso kuganiza.+ Ndipo adzaweruza mogwirizana ndi uthenga wabwino umene ndikulalikira.