Yohane 5:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Atate saweruza munthu aliyense, koma wapereka udindo wonse woweruza kwa Mwana,+ Machitidwe 10:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Ndiponso, anatilamula kuti tilalikire kwa anthu ndi kupereka umboni wokwanira+ woti iyeyu ndi amene Mulungu anamupatsa udindo woweruza anthu amoyo ndi akufa.+ 1 Petulo 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma anthu amenewa adzayankha mlandu kwa Khristu yemwe adzaweruze amoyo ndi akufa omwe.+
42 Ndiponso, anatilamula kuti tilalikire kwa anthu ndi kupereka umboni wokwanira+ woti iyeyu ndi amene Mulungu anamupatsa udindo woweruza anthu amoyo ndi akufa.+