Yohane 5:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Atate saweruza munthu aliyense, koma wapereka udindo wonse woweruza kwa Mwana,+ Machitidwe 10:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Ndiponso, anatilamula kuti tilalikire+ kwa anthu ndi kupereka umboni wokwanira wakuti iyeyu ndi Amene Mulungu anamuika kukhala woweruza anthu amoyo ndi akufa.+ Machitidwe 17:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Chifukwa wakhazikitsa tsiku limene akufuna kudzaweruza+ m’chilungamo dziko lapansi kumene kuli anthu, kudzera mwa munthu amene iye wamuika. Ndipo wapereka chitsimikizo kwa anthu onse mwa kumuukitsa+ kwa akufa.”
42 Ndiponso, anatilamula kuti tilalikire+ kwa anthu ndi kupereka umboni wokwanira wakuti iyeyu ndi Amene Mulungu anamuika kukhala woweruza anthu amoyo ndi akufa.+
31 Chifukwa wakhazikitsa tsiku limene akufuna kudzaweruza+ m’chilungamo dziko lapansi kumene kuli anthu, kudzera mwa munthu amene iye wamuika. Ndipo wapereka chitsimikizo kwa anthu onse mwa kumuukitsa+ kwa akufa.”