Luka 8:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chilichonse chobisidwa+ chidzaonekera poyera. Ndipo zinthu zonse zosungidwa mwachinsinsi kwambiri zidzadziwika ndi kuululika.+ 1 Timoteyo 5:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Momwemonso, ntchito zabwino zimaonekera poyera,+ ndipo ngakhale kuti zisaonekere sizingabisike mpaka kalekale.+
17 Chilichonse chobisidwa+ chidzaonekera poyera. Ndipo zinthu zonse zosungidwa mwachinsinsi kwambiri zidzadziwika ndi kuululika.+
25 Momwemonso, ntchito zabwino zimaonekera poyera,+ ndipo ngakhale kuti zisaonekere sizingabisike mpaka kalekale.+