10 Pakuti mtima wa aliyense wa ife udzaonekera pamaso pa mpando woweruzira milandu wa Khristu,+ kuti aliyense alandire mphoto yake pa zinthu zimene anachita ali m’thupi, mogwirizana ndi zimene anali kuchita, zabwino kapena zoipa.+
6 Ndipotu, pa chifukwa chimenechi uthenga wabwino unalengezedwanso kwa akufa,+ kuti aweruzidwe mwa thupi mogwirizana ndi kuona kwa anthu,+ koma akhale ndi moyo mwa mzimu+ mogwirizana ndi kuona kwa Mulungu.