Akolose 3:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 chifukwa mukudziwa kuti mudzalandira cholowa+ kuchokera kwa Yehova+ monga mphoto yanu. Tumikirani Ambuye wanu, Khristu, monga akapolo.+ Chivumbulutso 22:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “‘Taonani! Ndikubwera mofulumira,+ ndipo mphoto+ ndili nayo, yoti ndipereke kwa aliyense malinga ndi ntchito yake.+
24 chifukwa mukudziwa kuti mudzalandira cholowa+ kuchokera kwa Yehova+ monga mphoto yanu. Tumikirani Ambuye wanu, Khristu, monga akapolo.+
12 “‘Taonani! Ndikubwera mofulumira,+ ndipo mphoto+ ndili nayo, yoti ndipereke kwa aliyense malinga ndi ntchito yake.+