Mateyu 8:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma Yesu anamuyankha kuti: “Iwe unditsatirebe ine, ndipo aleke akufa aike akufa awo.”+ Aefeso 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiponso, Mulungu anapangitsa inuyo kukhala amoyo pamene munali akufa chifukwa cha zolakwa zanu ndi machimo anu.+
2 Ndiponso, Mulungu anapangitsa inuyo kukhala amoyo pamene munali akufa chifukwa cha zolakwa zanu ndi machimo anu.+