Mateyu 8:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma Yesu anamuyankha kuti: “Iwe unditsatirebe ine, ndipo aleke akufa aike akufa awo.”+ Akolose 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndiponso, ngakhale kuti munali akufa m’machimo anu ndipo munali osadulidwa, Mulungu anakupatsani moyo kuti mukhale ogwirizana ndi Khristu,+ ndipo anatikhululukira machimo athu onse motikomera mtima.+ 1 Timoteyo 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma amene amatsatira zilakolako zake kuti azikhutiritse,+ ndi wakufa+ ngakhale kuti ali ndi moyo. 1 Petulo 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndipotu, pa chifukwa chimenechi uthenga wabwino unalengezedwanso kwa akufa,+ kuti aweruzidwe mwa thupi mogwirizana ndi kuona kwa anthu,+ koma akhale ndi moyo mwa mzimu+ mogwirizana ndi kuona kwa Mulungu.
13 Ndiponso, ngakhale kuti munali akufa m’machimo anu ndipo munali osadulidwa, Mulungu anakupatsani moyo kuti mukhale ogwirizana ndi Khristu,+ ndipo anatikhululukira machimo athu onse motikomera mtima.+
6 Ndipotu, pa chifukwa chimenechi uthenga wabwino unalengezedwanso kwa akufa,+ kuti aweruzidwe mwa thupi mogwirizana ndi kuona kwa anthu,+ koma akhale ndi moyo mwa mzimu+ mogwirizana ndi kuona kwa Mulungu.