Salimo 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chonde, thetsani kuipa kwa anthu oipa,+Ndipo khazikitsani wolungama.+Mulungu pokhala wolungama+ akuyesa mtima+ ndi impso.+ Salimo 90:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Zolakwa zathu mwaziika patsogolo panu,+Ndipo machimo athu obisika* ali patsogolo pa nkhope yanu yowala.+ Miyambo 15:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Manda ndiponso malo a chiwonongeko+ zili pamaso pa Yehova.+ Ndiye kuli bwanji mitima ya ana a anthu?+
9 Chonde, thetsani kuipa kwa anthu oipa,+Ndipo khazikitsani wolungama.+Mulungu pokhala wolungama+ akuyesa mtima+ ndi impso.+
8 Zolakwa zathu mwaziika patsogolo panu,+Ndipo machimo athu obisika* ali patsogolo pa nkhope yanu yowala.+
11 Manda ndiponso malo a chiwonongeko+ zili pamaso pa Yehova.+ Ndiye kuli bwanji mitima ya ana a anthu?+