Levitiko 26:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Otsala pakati panu, adzazunzika+ chifukwa cha zolakwa zawo m’mayiko a adani awo. Iwo adzazunzika chifukwa cha zolakwa za makolo awo,+ mmene makolowo anazunzikira. Salimo 50:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Wachita zinthu zonsezi, koma ine ndinakhala chete.+Unali kuganiza kuti ine ndikhala ngati iwe.+Ine ndidzakudzudzula,+ ndipo ndidzaika machimo ako onse poyera iwe ukuona.+ Yeremiya 16:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pakuti maso anga akuona njira zawo zonse. Anthuwo sanabisike kwa ine, ndipo zolakwa zawo sizinabisike pamaso panga.+
39 Otsala pakati panu, adzazunzika+ chifukwa cha zolakwa zawo m’mayiko a adani awo. Iwo adzazunzika chifukwa cha zolakwa za makolo awo,+ mmene makolowo anazunzikira.
21 Wachita zinthu zonsezi, koma ine ndinakhala chete.+Unali kuganiza kuti ine ndikhala ngati iwe.+Ine ndidzakudzudzula,+ ndipo ndidzaika machimo ako onse poyera iwe ukuona.+
17 Pakuti maso anga akuona njira zawo zonse. Anthuwo sanabisike kwa ine, ndipo zolakwa zawo sizinabisike pamaso panga.+