Numeri 23:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mulungu si munthu, woti anganene mabodza,+Si mwana wa munthu, woti angadzimve kuti ali ndi mlandu.+Kodi ananenapo kanthu koma osachita,Analankhulapo kanthu kodi koma osakwaniritsa?+ Salimo 73:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iwo anena kuti: “Mulungu angadziwe bwanji?+Kodi Wam’mwambamwamba akudziwa zimenezi?”+ Salimo 94:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iwo amanena kuti: “Ya sakuona,+Ndipo Mulungu wa Yakobo sakudziwa zimene zikuchitika.”+ Mlaliki 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ngakhale woipa atachita zoipa+ maulendo 100 n’kukhala ndi moyo wautali akuchitabe zofuna zake, ine ndikudziwa kuti anthu amene amaopa Mulungu woona zidzawayendera bwino,+ chifukwa chakuti anali kumuopa.+
19 Mulungu si munthu, woti anganene mabodza,+Si mwana wa munthu, woti angadzimve kuti ali ndi mlandu.+Kodi ananenapo kanthu koma osachita,Analankhulapo kanthu kodi koma osakwaniritsa?+
12 Ngakhale woipa atachita zoipa+ maulendo 100 n’kukhala ndi moyo wautali akuchitabe zofuna zake, ine ndikudziwa kuti anthu amene amaopa Mulungu woona zidzawayendera bwino,+ chifukwa chakuti anali kumuopa.+